<
Maziko a abale Mchiyembeke zo
Mwalandiridwa pa website yathu.
TEAM MEMBERS IN MALAŵI
:
THE BOARD MEMBERS IN HOLLAND:
THE PERMANENT VOLUNTEER[S] IN HOLLAND [update list 2009]:
'Stichting Partners in Hoop', The Netherlands idayambaika pa 7 August 2006.
Bungweli lidalembetsa ku Notary Frantzen ndi ku Van Sisseren, ku Goes, Netherlands.
Bungweli lidalembetsedwa ku Chambewr ya Commerce ya Zeeland.
1. Cholinga cha bungweli
2. Bungweli likwaniritsa chikhumbo chake pa kulenga mgwirizano pakati pa anthu a ku Netherlands ndi Malaŵi kudzera mu zochitikazinso ndi
kuthekera kopeza ndalama za zolinga zazokhalzikitsidwazo. Bungweli silidakhazikike pakupeza phindu landalama.
Kulongosola za m’mene dzina lokuti abale muchiyembekezo lidayambira kukhulupirira kwa mulungu ndi chilimbikitso champhamvu ya bungweli ndi kulimbikira
kwa anthu aku Malaŵi. Mu umoyo wathu wachikhrisitu(kutsukika zamoyo) tikukhulupilira kuti tili ndi udindo ndi cholinga kusamalirana wina ndi mnzake
ndikuthandiza ofooka ndi osowa mudziko la Malaŵi. Chikhulupiliro chathu mwa Mulungu chimafuna kutengapo mbali pochita kanthu osangoti udindo wa kuuzimu wokha ayi.
Choncho chikhulupiliro chathu kwa Mulungu sichongoyima pawekha koma kuyendera limodzi ndi machitidwe athu (kugwirizana ndi mawu), Pachifukwa chimenechi,
tizipeleka tokha kwa a Malaŵi, kupeleka chithandizo choyenera mumzinda wabwino ndi kudziko monga Mulungu afunira. Zonsezi zikuyenera kukhazikika pa kulimbikira maubwenzi.
Pachifukwa cha zinthu izi, tasankha dzina lakuti abale muchiyembekezo. Zokhumba ndi ulemu zomwe tikuyang’anitsitsa zikuonekera zokha mudzinali.
Liwu loti partners (abale) likulongosola za umodzi, kutenga mbali ndi kuzipeleka, kupanga zinthu limodzi, kukhala m’modzi wagululo.
Liwu lokuit hope (chiyembekezo) likulongosola az kukhala ndi zokometsera kapena kudya zoyembezera zabwino. Kunena kwabwino muchidule ndi kwakuti
‘Chiyembekezo chapeza moyo’ choncho tinganene kuti chiyembekezo chimayendera limodzi ndi moyo pachifukwa chimenechi, timalemba chiyembekezo ndi chilembo chachikulu,
kutanthauza kuti “Opereka Moyo” (Mulungu Mwini)
© www.partnersinhoop.nl
David, Elizabeth, Billy, Zwaantje
James, Mishek, Shyreen, Mswera.
Thijs, Ronald, Jack, Paul.
Bernardine